Masalmo 78:38 BL92

38 Koma Iye pokhala ngwa cifundo,Anakhululukira coipa, osawaononga;Nabweza mkwiyo wace kawiri kawiri,Sanautsa ukali wace wonse.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 78

Onani Masalmo 78:38 nkhani