9 Tithandizeni Mulungu wa cipulumutso cathu,Cifukwa ca ulemerero wa dzina lanu;Ndipo tilanditseni, ndi kutifafanizira zoipa zathu,Cifukwa ca dzina lanu.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 79
Onani Masalmo 79:9 nkhani