1 Yimbitsirani Mulungu ndiye mphamvu yathu;Pfuulirani kwa Mulungu wa Yakobo.
2 Utsani Salimo, bwera nakoni kalingaka,Zeze wokondwetsa pamodzi ndi cisakasa.
3 Ombani lipenga, pokhala mwezi,Utakula mwezi, tsiku la phwando lathu.
4 Pakuti ici ndi colemba ca kwa Israyeli,Ciweruzo ca Mulungu wa Yakobo.