1 Mulungu aima mu msonkhano wa Mulungu,Aweruza pakati pa milungu.
2 Mudzaweruza mosalunjika kufikira liti,Ndi kusamalira nkhope ya oipa?
3 Weruzani osauka ndi amasiye;Weruzani molungama ozunzika ndi osowa.
4 Pulumutsani osauka ndi aumphawi:Alanditseni m'dzanja la oipa,