Masalmo 85:8 BL92

8 Ndidzamva colankhula Mulungu Yehova;Pakuti adzalankhula zamtendere ndi anthu ace, ndi okondedwa ace;Koma asabwererenso kucita zapusa.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 85

Onani Masalmo 85:8 nkhani