16 Mundibwerere ine, ndi kundicitira cifundo;Mpatseni mtumiki wanu mphamvu yanu,Ndipo pulumutsani mwana wa mdzakazi wanu.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 86
Onani Masalmo 86:16 nkhani