2 Sungani moyo wanga pakuti ine ndine wokondedwa wanu;Inu Mulungu wanga, pulumutsani mtumiki wanu wokhulupirira Inu.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 86
Onani Masalmo 86:2 nkhani