1 Maziko ace ali m'mapiri oyera.
2 Yehova akonda zipata za ZiyoniKoposa zokhalamo zonse za Yakobo.
3 Mudzi wa Mulungu, inu,Akunenerani zakukulemekezani.
4 Ndidzachula Rahabu ndi Babulo kwa iwo ondidziwa Ine;Taonani, Filistiya ndi Turo pamodzi ndi Kusi;Uyu anabadwa komweko.
5 Ndipo adzanena za Ziyoni,Uyu ndi uyo anabadwa m'mwemo;Ndipo Wam'mwambamwamba ndiye aclzaukhazikitsa.
6 Yehova adzawerenga, polembera mitundu ya anthu.Uyu anabadwa komweko.
7 Ndipo oyimba ndi oomba omwe adzati,Akasupe ansa onse ali mwa inu.