19 Pamenepo munalankhula m'masompenya ndi okondedwa anu,Ndipo mudati, Ndasenza thandizo pa ciphona;Ndakweza wina wosankhika mwa anthu.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 89
Onani Masalmo 89:19 nkhani