26 Iye adzandichula, ndi kuti, Inu ndinu Atate wanga,Mulungu wanga, ndi thanthwe la cipulumutso canga.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 89
Onani Masalmo 89:26 nkhani