1 Ndidzayamika Yehova ndi mtima wanga wonse;Ndidzawerengera zodabwiza zanu zonse.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 9
Onani Masalmo 9:1 nkhani