5 Mwadzudzula amitundu, mwaononga woipayo,Mwafafaniza dzina lao ku nthawi Yomka muyaya.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 9
Onani Masalmo 9:5 nkhani