Masalmo 90:10 BL92

10 Masiku a zaka zathu ndiwo zaka makumi asanu ndi awiri,Kapena tikakhala nayo mphamvudi zaka makumi asanu ndi atatu;Koma teronso kukula kwao kumati cibvuto ndi copanda pace;Pakuti kumapitako msanga ndipo tithawa ife tomwe.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 90

Onani Masalmo 90:10 nkhani