13 Udzaponda mkango ndi mphiri;Udzapondereza msona wa mkango ndi cinjoka:
14 Popeza andikondadi ndidzampulumutsa;Ndidzamkweza m'mwamba, papeza adziwa dzina langa.
15 Adzandipfuulira Ine ndipo ndidzamyankha;Kunsautso ndidzakhala naye pamodzi;Ndidzamlanditsa, ndi kumcitira ulemu.
16 Ndidzamkhutitsa ndi masiku ambiri,Ndi kumuonetsera cipulumutso canga,