Masalmo 95:10 BL92

10 Zaka makumi anai mbadwo uwu unandimvetsa cisoni,Ndipo ndinati, Iwo ndiwo anthu osokerera mtima,Ndipo sadziwa njira zanga.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 95

Onani Masalmo 95:10 nkhani