3 Anakumbukila cifundo cace ndi cikhulupiriko cace ku nyumba ya Israyeli;Malekezero onse a dziko lapansi anaona cipulumutso ca Mulungu wathu.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 98
Onani Masalmo 98:3 nkhani