Masalmo 98:9 BL92

9 Pamaso pa Yehova, popeza akudza kudzaweruza dziko lapansi;Adzaweruza dziko lokhalamo anthu ndi cilungamo,Ndi mitundu ya anthu molunjika,

Werengani mutu wathunthu Masalmo 98

Onani Masalmo 98:9 nkhani