5 Kuti ndione cokomaco ca osankhika anu,Kuti ndikondwere naco cikondwerero ca anthu anu,Kuti ndidzitamandire pamodzi ndi colowa canu.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 106
Onani Masalmo 106:5 nkhani