Masalmo 11:6 BL92

6 Adzagwetsa pwata pwata misampha pa oipa;Moto ndi miyala yasuifure, ndi mphepo yoopsa zidzawagawikira m'cikho cao.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 11

Onani Masalmo 11:6 nkhani