Masalmo 115:1 BL92

1 Kwa ife ai, Yehova, kwa ife ai, Koma kwa dzina lanu patsani ulemerero,Cifukwa ca cifundo canu, ndi coonadi canu.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 115

Onani Masalmo 115:1 nkhani