14 Ndidzacitazowindazanga za kwa Yehova,Tsopano, pamaso pa anthu ace onse.
15 Imfa ya okondedwa aceNja mtengo wace pamaso pa Yehova.
16 Ndiloleni, Yehova, indetu ndine mtumiki wanu;Ndine mtumiki wanu, mwana wa mdzakazi wanu;Mwandimasulira zondimanga,
17 Ndidzapereka kwa Inu nsembe yaciyamiko,Ndipo ndidzaitanira dzina la Yehova.
18 Ndidzacita zowinda zanga za kwa Yehova,Tsopano, pamaso pa anthu ace onse;
19 M'mabwalo a nyumba ya Yehova,Pakati pa inu, Yerusalemu. Haleluya.