7 Akweza mitambo icokere ku malekezero a dziko lapansi;Ang'animitsa mphezi zidzetse mvula;Aturutsa mphepo mosungira mwace.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 135
Onani Masalmo 135:7 nkhani