Masalmo 135:6 BL92

6 Ciri conse cimkonda Yehova acicita,Kumwamba ndi pa dziko lapansi, m'nyanja ndi mozama monse.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 135

Onani Masalmo 135:6 nkhani