Masalmo 144:12 BL92

12 Kuti ana athu amuna akhale ngati mmera udakula usanakhwime;Ana athu akazi ngati nsanamira za kungondya, zosema zikometsere nyumba ya mfumu.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 144

Onani Masalmo 144:12 nkhani