Masalmo 144:13 BL92

13 Kuti nkhokwe zathu zidzale, kutipatsa za mitundu mitundu;Ndi kuti nkhosa zathu ziswane zikwi zikwi, inde zikwi khumi kubusako.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 144

Onani Masalmo 144:13 nkhani