Masalmo 146:9 BL92

9 Yehova asunga alendo;Agwiriziza mwana wamasiye mkazi wamasiye;Koma akhotetsa njira ya oipa.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 146

Onani Masalmo 146:9 nkhani