5 Tidzapfuula mokondwera mwa cipulumutso canu,Ndipo m'dzina la Mulungu wathu tidzakweza mbendera:Yehova akwaniritse mapempho ako onse.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 20
Onani Masalmo 20:5 nkhani