6 Tsopano ndidziwa kuti Yehova apulumutsa wodzozedwa wace;Adzambvomereza m'Mwamba mwace moyeraNdi mphamvu ya cipulumutso ca dzanja lace lamanja.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 20
Onani Masalmo 20:6 nkhani