Masalmo 22:1 BL92

1 Mulungu wanga, Mulungu wanga, mwandisiyiranji ine?Mukhaliranji kutali kwa cipulumutso canga, ndi kwa mau a kubuula kwanga?

Werengani mutu wathunthu Masalmo 22

Onani Masalmo 22:1 nkhani