6 Inde ukoma ndi cifundo zidzanditsata masiku onse a moyo wanga:Ndipo ndidzakhala m'nyumba ya Yehova masiku onse.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 23
Onani Masalmo 23:6 nkhani