Masalmo 27:5 BL92

5 Cifukwa kuti pa dzuwa la tsoka Iye adzandibisa mumsasa mwace:Adzandibisa m'tsenjezi mwa cihema cace;Pathanthwe adzandikweza.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 27

Onani Masalmo 27:5 nkhani