Masalmo 27:6 BL92

6 Ndipo tsopano mutu wanga udzakwezeka pamwamba pa adani anga akundizinga;Ndipo ndidzapereka m'cihema mwace nsembe za kupfuula mokondwera;Ndidzayimba, inde, ndidzayimbira Yehova zomlemekeza.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 27

Onani Masalmo 27:6 nkhani