5 Pakuti mkwiyo wace ukhala kanthawi kokha;Koma kuyanja kwace moyo wonse:Kulira kucezera,Koma mamawa kuli kupfuula kukondwera.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 30
Onani Masalmo 30:5 nkhani