Masalmo 35:13 BL92

13 Koma ine, pakudwala iwowa, cobvala canga ndi ciguduli:Ndinazunza moyo wanga ndi kusala;Ndipo pemphero langa linabwera ku cifuwa canga.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 35

Onani Masalmo 35:13 nkhani