14 Ndakhala ine monga ngad iye anali bwenzi langa, kapena mbale wanga:Polira ndinaweramira pansi, monga munthu wakulira maliro amai wace.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 35
Onani Masalmo 35:14 nkhani