26 Acite manyazi, nadodome iwo akukondwera cifukwa ca coipa cidandigwera:Abvekeke ndi manyazi ndi kupunzika iwo akudzikuza pa ine.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 35
Onani Masalmo 35:26 nkhani