27 Apfuule mokondwera nasangalale iwo akukondwera naco cilungamo canga:Ndipo anene kosalekeza, Abuke Yehova,Amene akondwera ndi mtendere wa mtumiki wace.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 35
Onani Masalmo 35:27 nkhani