6 Cilungamo canu cikunga mapiri a Mulungu;Maweruzo anu akunga cozama cacikuru:Yehova, musunga munthu ndi nyama.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 36
Onani Masalmo 36:6 nkhani