3 Mumnofu mwanga mulibe camoyo cifukwa ca ukali wanu;Ndipo m'mafupa anga simuzizira, cifukwa ca colakwa canga.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 38
Onani Masalmo 38:3 nkhani