4 Pakuti mphulupulu zanga zapitirira pamutu panga:Ndathodwa nazo monga ndi katundu wolemera.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 38
Onani Masalmo 38:4 nkhani