2 Moyo wanga uli ndi ludzu la kwa Mulungu, la kwa Mulungu wamoyo:Ndikadze liti kuoneka pamaso pa Mulungu?
Werengani mutu wathunthu Masalmo 42
Onani Masalmo 42:2 nkhani