8 Yehova, munditsogolere m'cilungamo canu, cifukwa ca akundizondawo;Mulungamitse njira yanu pamaso panga.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 5
Onani Masalmo 5:8 nkhani