9 Pakuti m'kamwa mwao mulibe mau okhazikika;M'kati mwao m'mosakaza;M'mero mwao ndi manda apululu:Lilime lao asyasyalika nalo.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 5
Onani Masalmo 5:9 nkhani