4 Moyo wanga uli pakati pa mikango;Ndigona pakati pa oyaka moto,Ndiwo ana a anthu amene mano ao ali nthungo ndi mibvi,Ndipo lilime lao ndilio lupanga lakuthwa.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 57
Onani Masalmo 57:4 nkhani