Masalmo 57:3 BL92

3 Adzanditumizira m'mwamba, nadzandipulumutsaPonditonza wofuna kundimeza;Mulungu adzatumiza cifundo cace ndi coonadi cace.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 57

Onani Masalmo 57:3 nkhani