5 Koma ine ndine wozunzika ndi waumphawi;Mundifulumirire, Mulungu:Inu ndinu mthandizi wanga ndi mpulumutsi wanga;Musacedwe, Yehova.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 70
Onani Masalmo 70:5 nkhani