13 Potero ife anthu anu ndi nkhosa za pabusa panuTidzakuyamikani kosatha;Tidzafotokozera cilemekezo canu ku mibadwo mibadwo.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 79
Onani Masalmo 79:13 nkhani