10 Anenerenji amitundu, Ali kuti Mulungu wao?Kubwezera cilango ca mwazi wa atumiki anu umene anaukhetsaKudziwike pakati pa amitundu pamaso pathu,
11 Kubuula kwa wandende kufike kuli Inu;Monga mwa mphamvu yanu yaikuru lolani ana a imfa atsale;
12 Ndipo anansi athu amene anatonza Inu muwabwezere cotonza cao,Kasanu ndi kawiri kumtima kwao, Ambuye.
13 Potero ife anthu anu ndi nkhosa za pabusa panuTidzakuyamikani kosatha;Tidzafotokozera cilemekezo canu ku mibadwo mibadwo.