7 Unaitana posautsika, ndipo ndinakulanditsa;Ndinakubvomereza mobisalika m'bingu;Ndinakuyesa ku madzi a Meriba.
Werengani mutu wathunthu Masalmo 81
Onani Masalmo 81:7 nkhani