Masalmo 93:1 BL92

1 Yehova acita ufumu; wadzibveka ndi ukulu;Wadzibveka Yehova, wadzimangirira mphamvu m'cuuno;Dziko lomwe lokhalamo anthu likhazikika, silidzagwedezeka.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 93

Onani Masalmo 93:1 nkhani